INTRODUCTION – Chichewa to English Phrasebook
What is your name?*Dzina lanu ndani?
My name is Cedric and yours?*Dzina langa ndi Susan .
Happy to meet you!*Ndakondwa kukumana ndi inu
Happy to meet you too!*Ndakondwa kukumananso ndi inu
Where are you from?*Mumachokera kuti?
. I am from USA.*Ndimachokera ku USA
What is your job? / What do you do?*Mumagwira ntchito yanji?
I do work of a volunteer*Ndimagwira ntchito yodzipereka
I learning to speak Chichewa*Ndikuphunzira kulankhula chichewa
Where will you stay?*Mudzakhala kuti?
I will stay in Dedza*Ndidzakhala ku Dedza
Thanks see you later*Zikomo tiwonana
Leave a Reply