BASIC NEEDS – Chichewa to English Phrasebook
tired.*Ndatopa
I am hungry.*Ndili ndi njala
I am full.*Ndakhuta
I am thirsty .*Ndili ndi ludzu
Where is the toilet?*Chimbudzi chili kuti?
I want to drink water*Ndikufuna kumwa madzi.
I want to sleep.*Ndikufuna kugona
I want to eat .*Ndikufuna kudya
Iam feeling hot*Ndikumva kutentha
I am feeling cold*Ndikumva kuzizira
Toilet*Chimbudzi
Shower room*Bafa
I want to bathe*Ndikufuna kusamba
I don’t like meat.*Sindimakonda nyama
How do you say ……..in Chichewa?*Mumati chiyani………mu Chichewa?
Leave a Reply