Category: Chichewa to English Phrasebook

  • RELATIONS – Chichewa to English Phrasebook

    RELATIONS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Family*Banja
    Father*Bambo
    Mother*Mayi
    Brother*Achimwene
    Sister*Achemwali
    Grand father*Agogo amuna
    Grand mother*Agogo akazi
    Children*Ana
    To be married*Kukwatira/kukwatiwa
    Single child*Mwana m`modzi
    Twins*Mapasa
    Boy/girlfriend*Chibwenzi
    My friend*Mzanga

  • QUESTIONING WORDS – Chichewa to English Phrasebook

    QUESTIONING WORDS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Who?*Ndani?
    Where?*Kuti?
    What?*Chiyani?
    How many?*Angati?
    What time?*Nthawi yanji?
    When?*Liti?
    How much?*Ndalama zingati?
    Why?*Chifukwa chiyani?
    How?*Bwanji
    Because*Chifukwa?

  • PARTS OF THE DAY – Chichewa to English Phrasebook

    PARTS OF THE DAY – Chichewa to English Phrasebook

     

    Morning*M`mawa
    Noon*Masana
    Evening*Usiku

  • BASIC NEEDS – Chichewa to English Phrasebook

    BASIC NEEDS – Chichewa to English Phrasebook

     

    tired.*Ndatopa
    I am hungry.*Ndili ndi njala
    I am full.*Ndakhuta
    I am thirsty .*Ndili ndi ludzu
    Where is the toilet?*Chimbudzi chili kuti?
    I want to drink water*Ndikufuna kumwa madzi.
    I want to sleep.*Ndikufuna kugona
    I want to eat .*Ndikufuna kudya
    Iam feeling hot*Ndikumva kutentha
    I am feeling cold*Ndikumva kuzizira
    Toilet*Chimbudzi
    Shower room*Bafa
    I want to bathe*Ndikufuna kusamba
    I don’t like meat.*Sindimakonda nyama
    How do you say ……..in Chichewa?*Mumati chiyani………mu Chichewa?

  • COMMANDS AND REQUESTS – Chichewa to English Phrasebook

    COMMANDS AND REQUESTS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Please eat*Idyani
    Please sit*Khalani
    ! Come here!*Bwerani kuno
    Please wait*Dikirani!
    Let’s go/come on!*Tiyeni!
    False / untrue*Bodza
    True*Zowona
    That’s enough!*Basi!
    Do you understand?*Mukumvetsa?
    I need_(coke)_ please.*Ndikufuna coke chonde
    Ndipatseni madzi chonde. Give me _(water)_ please.*Give me _(water)_ please.
    Go well*Pitani bwino

  • HOUSEHOLD ITEMS – Chichewa to English Phrasebook

    HOUSEHOLD ITEMS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Chair*Mpando
    Table*Tebulo
    Bed frame*Kama
    Blankets*Zofunda
    Door*Chitseko
    Window*Zenera
    Mosquito net*Chotetezera udzudzu
    Matt*Mphasa
    Broom*Tsache

  • DAYS OF THE WEEK – Chichewa to English Phrasebook

    DAYS OF THE WEEK – Chichewa to English Phrasebook

     

    Monday*Lolemba
    Tuesday*Lachiwiri
    Wednesday*Lachitatu
    Thursday*Lachinayi
    Friday*Lachisanu
    Saturday*Loweluka
    Sunday*Lamulungu
    Yesterday*Dzulo
    Today*Lero
    Tomorrow*Mawa

  • NUMBERS – Chichewa to English Phrasebook

    NUMBERS – Chichewa to English Phrasebook

     

    1 One *-Modzi
    2 Two *-Wiri
    3 Three *-tatu
    4 Four *-nayi
    5 Five *-sanu
    6 – Six *Sanu ndi modzi
    7 Seven *-sanu ndi wiri
    8 – Eight *Sanu ndi tatu
    9 Nine *-sanu ndi nayi
    10 Ten *Khumi

  • INTRODUCTION – Chichewa to English Phrasebook

    INTRODUCTION – Chichewa to English Phrasebook

     

    What is your name?*Dzina lanu ndani?
    My name is Cedric and yours?*Dzina langa ndi Susan .
    Happy to meet you!*Ndakondwa kukumana ndi inu
    Happy to meet you too!*Ndakondwa kukumananso ndi inu
    Where are you from?*Mumachokera kuti?
    . I am from USA.*Ndimachokera ku USA
    What is your job? / What do you do?*Mumagwira ntchito yanji?
    I do work of a volunteer*Ndimagwira ntchito yodzipereka
    I learning to speak Chichewa*Ndikuphunzira kulankhula chichewa
    Where will you stay?*Mudzakhala kuti?
    I will stay in Dedza*Ndidzakhala ku Dedza
    Thanks see you later*Zikomo tiwonana

  • LIKING – Chichewa to English Phrasebook

    LIKING – Chichewa to English Phrasebook

     

    Ndi konda iwe (you).*I like you.
    Kodi, mu ndi konda ine?*Do you like me?
    Inde, ndi konda iwe.*Yes, I like you.
    Kodi, mu konda ndalama?*Do you like money?
    Inde, ndi konda ndalama (money).*Yes, I like money
    Ndi konda madzi (water).*I like water.
    Mu konda modzi?.*You like water.
    Ndi konda abuku.*I like some books.
    A konda galimoto (car).*He likes the car.
    Ayi sai konda galimoto.*She does not like the car.
    Kodi, mu konda chakudya cha madzulo (dinner).*Do you like the dinner?
    Si, ndi konda chakudya cha madzulo.*No, I do not like the dinner.
    Oh. zoipa. Ipa-ipa! Oh.*Darn! Mate!
    Chonde, musati Ipa-ipa.*Please do not say Mate!