EVERYTHING – Chichewa to English Phrasebook
Ndi li pano.*I am here.
U/Mu li apo.*You are there.
Ndi konda iwe/inu.*I like you.
U/Mu konda ndalama.*You like the money.
A/ma chita ichi.*He does this.
A machita icho*She does that.
Ndi tha ku-lankhula pong’ono Chichewa!*I can speak a little Chichewa!
Si u nga nene Ipa-ipa.*You can not say Mate?
Ndi kumvetsa iwe/inu (you).*I understand you.
Si mu ndi mvetsa ine (me).*You do not understand me.
Ndi funa ku-pita ku bar (mowa).*I want to go to the bar.
U/Mu funa ku-pita ku chimbudzi (toilet).*You want to go to the toilet.
Ndi li ndi nthawi, yochepa chemwali*I have a little time, Miss!
Koma muli ndi ndalama zochepa, a-bamba?*But, do you have a little money, Sir?
Chonde, osamwa madzi ku Fransi!!*Please don’t drink the water in France!!
Imwa vinyo.*Drink the wine.
uli bwanji, Eliza?*How are you, Eliza?
Ndi-li bwino, Zikomo.*I am well, thank you.
Ndi ya/cha chi kulu?*Is it big?
Ayi, ndi ka ka ng’ono.*No, it is small.
Si umu dziwa mzimayi !*You do not know her!
zoipa. A li osanagalatsa!*Darn! She is wonderful!
Inde, tsopano, ndi li ndi mavuto asanu*Yes now, I have five problems!!!
Ana onse!*All the children!
Ndi chain icho?*What is that?
Pepani. Chani?*Pardon. What?
Iyo apo.*There it is.
Si zo ipa.*Not bad.
Chabwino?*OK?
Inde, a li bwino.*Yes, it’s cool!
Inde, a li bwino.*Yes, it’s cool! (classy)
Inde, a li bwino.*Yes, it’s cool! (upper class)
Chonde, u/musanene ipa-ipai.*Please do not say Mate!
Ayi li bwino.*It is not upper class)!!!
Ndi yenala ku-chita ichi.*I must do this.
Mu yenala ku chita icho.*You must do that
zosangalatsa?*Wonderful?
Inde, mu li osangalatsa.*Yes you are wonderful!
Tsalanai bwino tsopano.*Bye bye, for now!
Tsala, tsopano.*Bye bye, for now!
Tsa lani bwino patsono.*Bye bye, for now!
Tionana posachedwa!*Be seeing you soon!!