Author: aznimi

  • COMMANDS AND REQUESTS – Chichewa to English Phrasebook

    COMMANDS AND REQUESTS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Please eat*Idyani
    Please sit*Khalani
    ! Come here!*Bwerani kuno
    Please wait*Dikirani!
    Let’s go/come on!*Tiyeni!
    False / untrue*Bodza
    True*Zowona
    That’s enough!*Basi!
    Do you understand?*Mukumvetsa?
    I need_(coke)_ please.*Ndikufuna coke chonde
    Ndipatseni madzi chonde. Give me _(water)_ please.*Give me _(water)_ please.
    Go well*Pitani bwino

  • BASIC NEEDS – Chichewa to English Phrasebook

    BASIC NEEDS – Chichewa to English Phrasebook

     

    tired.*Ndatopa
    I am hungry.*Ndili ndi njala
    I am full.*Ndakhuta
    I am thirsty .*Ndili ndi ludzu
    Where is the toilet?*Chimbudzi chili kuti?
    I want to drink water*Ndikufuna kumwa madzi.
    I want to sleep.*Ndikufuna kugona
    I want to eat .*Ndikufuna kudya
    Iam feeling hot*Ndikumva kutentha
    I am feeling cold*Ndikumva kuzizira
    Toilet*Chimbudzi
    Shower room*Bafa
    I want to bathe*Ndikufuna kusamba
    I don’t like meat.*Sindimakonda nyama
    How do you say ……..in Chichewa?*Mumati chiyani………mu Chichewa?

  • PARTS OF THE DAY – Chichewa to English Phrasebook

    PARTS OF THE DAY – Chichewa to English Phrasebook

     

    Morning*M`mawa
    Noon*Masana
    Evening*Usiku

  • QUESTIONING WORDS – Chichewa to English Phrasebook

    QUESTIONING WORDS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Who?*Ndani?
    Where?*Kuti?
    What?*Chiyani?
    How many?*Angati?
    What time?*Nthawi yanji?
    When?*Liti?
    How much?*Ndalama zingati?
    Why?*Chifukwa chiyani?
    How?*Bwanji
    Because*Chifukwa?

  • RELATIONS – Chichewa to English Phrasebook

    RELATIONS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Family*Banja
    Father*Bambo
    Mother*Mayi
    Brother*Achimwene
    Sister*Achemwali
    Grand father*Agogo amuna
    Grand mother*Agogo akazi
    Children*Ana
    To be married*Kukwatira/kukwatiwa
    Single child*Mwana m`modzi
    Twins*Mapasa
    Boy/girlfriend*Chibwenzi
    My friend*Mzanga

  • GETTING – Chichewa to English Phrasebook

    GETTING – Chichewa to English Phrasebook

     

    Chonde, patse ndalama (money),*Please give me the money.
    Chonde, tenga ndalama..*Please take the money.
    Ndi tenga ndalama.*I take the money.
    Chonde, patse tikiti.*Please give me the ticket.
    Chonde, tenga tikiti.*Please take the ticket.
    Ndi tenga tikiti.*I take the ticket.
    Chonde, patse ichi (thing).*Please give me the thing.
    Chi li kuti (where)?*Where is the thing?
    Si-ndi ku dziwa*I do not know.
    Chonde, patse mamuna/mzi bambo (man)!*Please give me a man
    Zoipa. . Mkazi li ti!*Darn-t!!! What a woman!!
    A li osangalatsa!*She is intertaining

  • WAITING – Chichewa to English Phrasebook

    WAITING – Chichewa to English Phrasebook

     

    Ndi funa (want).*I want.
    Ndi funa ku-dya pang’ono (a little).*I want to eat a little.
    Ndi funa ku-mwa madzi.*I want to drink water.
    Ndi funa ku-pita ku chiumbudzi (toilet) !!!!*I want to go to the toilet!!!
    Kodi, mu funa ku-dya pangono?*Do you want to eat a little?
    Iyayai, si ndi funa ku-dya*No, I do not want to eat.
    Zoipa, Ndi kufuna kuku-patsa pang’ono (some*Darn! I want to give you a bit.
    Iyayi, zikomo.*No, thank you.
    Ndi funa ku-bwera (come).*I want to come.
    Kodi, mu-funa ku gona ndi ine?*Do you want to sleep with me?
    Ayi Si, ndi funa ku-gona No,*I do not want to sleep.
    Miguel, kodi, mu funa ku-dya achule?*Miguel do you want to eat the frogs?
    Zoipa. Si tsopano, zikomo.*Darn! Not just now, thank you!
    Ti li osangalala!*We are wonderful

  • NUMBERING – Chichewa to English Phrasebook

    NUMBERING – Chichewa to English Phrasebook

     

    Ndi li ndi vuto li modzi*I have one problem.
    Inde, mu li ndi vuto limodzi*Yes, you have a problem.
    Ayi, mu li ndi mavuto awiri.*No, you have two (of them).
    A li ndi atatu.*He has three.
    A li ndi anai (4).*She has four.
    Ti li ndi asanu (5).*We have five.
    Kodi, mu li ndi asanu?*Do you have five?
    Inde, tsopono, ndi li ndi asanu!!*Yes now, I have five problems!!!
    Ana onse!*All the children!
    Ana ali/ndi osangalatsa!*Children are wondeful!

  • UNDERSTANDING – Chichewa to English Phrasebook

    UNDERSTANDING – Chichewa to English Phrasebook

     

    Ndi mvetsa.*I understand.
    si ndi mvetsa.*I do not understand.
    U/mu mvetsa.*You understand.
    siMu mvetsa (understand).*You do not understand.
    Kodi, muwa mvetsa a-kazi (women)?*Do you understand women?
    Ayi, ayi, si ndi a mvetsa iwo!!*No. No. I do not understand them!!!
    Oh. zoipa Oh.*Darn! Mate!
    Chonde musanene/musati Ipa-ipa ayi.*Please do not say Mate!
    Mu li osangalatsa!*You are intertaining!

  • COMMON WORDS – Chichewa to English Phrasebook

    COMMON WORDS – Chichewa to English Phrasebook

     

    Thank you*Zikomo
    Hello*Moni
    Mr.*A-Bambo
    Mrs.*A-Mayi
    Yes*Inde
    No*Iyay
    Good*Bwino?
    Please*Chonde
    Do you have?*Kodi mu li ndi…?
    Goodbye*Tsalani bwino
    See you soon!*Ndikuwona posachedwa
    Who?*Ndani?
    What?*Chani?
    I want*Ndi funa
    Where?*Kuti?
    today (lero)
    tomorrow (mawa)
    paper pepala)
    newspaper (gazeti/pepala)
    day*(tsiku)
    week*(mulungu)
    year*(chaka)
    hour*(hora)
    minute*(mphindi, many (ambiri)
    hamburger,*(hamburger)
    think*(ganiza)
    read*(werenga)
    write*(lemba)
    laugh*(seka)
    dance*(bvina)
    later*(patsogolo)
    stop*(ima)
    policeman*(polisi)
    six*(-zisanu ndi-chimodzi)
    seven*(zisanu ndi-ziwiri)
    eight*(zisanu ndi-zitatu)
    nine*(zisanu ndi-zinai)
    ten*(khumi)
    hundred*(zana)
    thousand*(chikwi)
    mate*(bwenzi)
    see you soon*(tionana posachedwa)